Face To Face - Chichewa Edition
US$1.50
15% OFF CODE: SAVE15
Description
MASO NDI MASO Kuyang'ana Mwa Uzimu Pa Moyo Wa Mose, Munthu Amene Mulungu Adamuona Maso Ndi Maso Panalibe mwamuna kapena mkazi amene anayenda pafupi ndi Mulungu monga Mose anachitira. Apa panali munthu amene anakhala masiku pamaso pa Mulungu. Analankhula ndi Mulungu maso ndi maso monga mmene timalankhulira ndi mnzathu. Moyo wake unali wodzala ndi umboni wozizwitsa wa kukhalapo kwa Mulungu. Kodi iye anali munthu wotani? Anali munthu ngati inu ndi ine. Iye anali kutali ndi ungwiro. Anavutika ndi ny